Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 15:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mudzawabweretsa nʼkuwakhazikitsa mʼphiri limene ndi cholowa chanu.+

      Malo okhazikika amene mwakonzeratu kuti mukhalemo, inu Yehova.

      Malo opatulika amene manja anu, inu Yehova, anakhazikitsa.

  • Salimo 78:55
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 55 Iye anathamangitsa mitundu ya anthu kuichotsa pamaso pawo.+

      Iye anawagawira dzikolo kuti likhale cholowa chawo pochita kuwayezera ndi chingwe.+

      Anachititsa mafuko a Isiraeli kuti akhale mʼnyumba zawozawo.+

  • Salimo 80:8, 9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Munachititsa kuti mtengo wa mpesa+ uchoke mu Iguputo.

      Munathamangitsa mitundu ya anthu kuti mudzalemo mtengowo.+

       9 Munalambula malo odzalapo mtengo wa mpesawo,

      Ndipo unazika mizu nʼkudzaza dziko.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena