Deuteronomo 4:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Anachotsa pamaso panu mitundu yaikulu ndi yamphamvu kuposa inu, kuti akulowetseni mʼdziko lawo nʼkukupatsani kuti likhale cholowa chanu ngati mmene zilili lero.+ Yoswa 24:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndinawachititsa mantha inu musanafike, choncho anakuthawani+ ngati mmene anachitira mafumu awiri a Aamori. Iwo sanathawe chifukwa cha lupanga lanu kapena chifukwa cha uta wanu.+
38 Anachotsa pamaso panu mitundu yaikulu ndi yamphamvu kuposa inu, kuti akulowetseni mʼdziko lawo nʼkukupatsani kuti likhale cholowa chanu ngati mmene zilili lero.+
12 Ndinawachititsa mantha inu musanafike, choncho anakuthawani+ ngati mmene anachitira mafumu awiri a Aamori. Iwo sanathawe chifukwa cha lupanga lanu kapena chifukwa cha uta wanu.+