Yoswa 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo ndinakufikitsani kudziko la Aamori amene ankakhala kutsidya lina* la Yorodano. Iwo anayamba kumenyana nanu+ koma ndinawapereka mʼmanja mwanu kuti mutenge dziko lawo kukhala lanu moti ndinawafafaniza pamaso panu.+
8 Ndipo ndinakufikitsani kudziko la Aamori amene ankakhala kutsidya lina* la Yorodano. Iwo anayamba kumenyana nanu+ koma ndinawapereka mʼmanja mwanu kuti mutenge dziko lawo kukhala lanu moti ndinawafafaniza pamaso panu.+