Salimo 48:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Munsanja zake zokhala ndi mpanda wolimba,Mulungu wasonyeza kuti iye ndi malo othawirako otetezeka.*+ Salimo 125:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mofanana ndi mapiri amene azungulira Yerusalemu,+Yehova wazungulira anthu ake,+Kuyambira panopa mpaka kalekale.
3 Munsanja zake zokhala ndi mpanda wolimba,Mulungu wasonyeza kuti iye ndi malo othawirako otetezeka.*+
2 Mofanana ndi mapiri amene azungulira Yerusalemu,+Yehova wazungulira anthu ake,+Kuyambira panopa mpaka kalekale.