Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 30:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Lero ndaika moyo ndi imfa, dalitso ndi temberero pamaso panu.+ Kumwamba ndi dziko lapansi ndi mboni pa zochita zanu. Choncho inuyo ndi mbadwa zanu+ musankhe moyo kuti mukhalebe ndi moyo.+

  • Deuteronomo 32:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 “Tamverani kumwamba inu, ndipo ine ndilankhula,

      Dziko lapansi limve mawu a pakamwa panga.

  • Yesaya 1:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Imvani inu okhala kumwamba, ndipo tcherani khutu inu okhala padziko lapansi,+

      Chifukwa Yehova wanena kuti:

      “Ndalera ana nʼkuwasamalira kuti akule,+

      Koma iwo andipandukira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena