Salimo 32:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamapeto pake ndinaulula tchimo langa kwa inu,Sindinabise cholakwa changa.+ Ndinati: “Ndidzaulula machimo anga kwa Yehova.”+ Ndipo inu munandikhululukira zolakwa zanga ndi machimo anga.+ (Selah) Salimo 40:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Masoka amene andizungulira ndi ambiri moti sindingathe kuwawerenga.+ Zolakwa zanga ndi zochuluka moti sindikutha kuona kumene ndikulowera.+Zachuluka kwambiri kuposa tsitsi lakumutu kwanga,Ndipo ndataya mtima.
5 Pamapeto pake ndinaulula tchimo langa kwa inu,Sindinabise cholakwa changa.+ Ndinati: “Ndidzaulula machimo anga kwa Yehova.”+ Ndipo inu munandikhululukira zolakwa zanga ndi machimo anga.+ (Selah)
12 Masoka amene andizungulira ndi ambiri moti sindingathe kuwawerenga.+ Zolakwa zanga ndi zochuluka moti sindikutha kuona kumene ndikulowera.+Zachuluka kwambiri kuposa tsitsi lakumutu kwanga,Ndipo ndataya mtima.