2 Samueli 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nʼchifukwa chiyani unanyoza mawu a Yehova pochita zoipa pamaso pake? Unapha Uriya Muhiti ndi lupanga.+ Kenako unatenga mkazi wake kuti akhale mkazi wako+ utapha Uriyayo ndi lupanga la Aamoni.+ Salimo 38:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndinaulula cholakwa changa.+Tchimo langa linkandisowetsa mtendere.+
9 Nʼchifukwa chiyani unanyoza mawu a Yehova pochita zoipa pamaso pake? Unapha Uriya Muhiti ndi lupanga.+ Kenako unatenga mkazi wake kuti akhale mkazi wako+ utapha Uriyayo ndi lupanga la Aamoni.+