Aroma 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ayi. Ngakhale munthu aliyense atakhala wabodza,+ Mulungu angapezekebe kuti ndi wonena zoona+ mogwirizana ndi zimene Malemba amanena kuti: “Mukamalankhula, mumalankhula zachilungamo kuti muwine pamene mukuweruzidwa.”+
4 Ayi. Ngakhale munthu aliyense atakhala wabodza,+ Mulungu angapezekebe kuti ndi wonena zoona+ mogwirizana ndi zimene Malemba amanena kuti: “Mukamalankhula, mumalankhula zachilungamo kuti muwine pamene mukuweruzidwa.”+