Numeri 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mulungu sali ngati munthu amene amanena mabodza,+Sali ngati mwana wa munthu amene amasintha maganizo.*+ Akanena kanthu, kodi angalephere kuchita? Akalankhula, kodi angalephere kukwaniritsa?+ Salimo 116:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nditapanikizika ndinati: “Munthu aliyense ndi wabodza.”+
19 Mulungu sali ngati munthu amene amanena mabodza,+Sali ngati mwana wa munthu amene amasintha maganizo.*+ Akanena kanthu, kodi angalephere kuchita? Akalankhula, kodi angalephere kukwaniritsa?+