Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 23:3, 4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Mulungu wa Isiraeli analankhula;

      Thanthwe la Isiraeli+ linandiuza kuti:

      ‘Munthu wolamulira anthu akakhala wachilungamo,+

      Nʼkumalamulira moopa Mulungu,+

       4 Zimakhala ngati kuwala kwa mʼmawa pamene dzuwa lawala,+

      Mʼmawa wopanda mitambo.

      Zimakhala ngati mvula yakata ndipo kwawala,

      Nʼkuchititsa msipu kumera padziko.’+

  • Salimo 119:105
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 105 Mawu anu ndi nyale younikira kumapazi anga,

      Komanso kuwala kounikira njira yanga.+

  • 1 Akorinto 13:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Panopa sitikuona bwinobwino chifukwa tikugwiritsa ntchito galasi losaoneka bwino, koma pa nthawiyo tizidzaona bwinobwino. Panopa sindikudziwa zonse, koma pa nthawiyo ndidzadziwa zonse ngati mmene Mulungu akundidziwira ineyo.

  • 2 Akorinto 4:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Popeza Mulungu ndi amene anati: “Kuwale kuchokera mumdima,”+ ndipo pogwiritsa ntchito nkhope ya Khristu waunika mitima yathu kuti iwale+ ndi ulemerero wokhudza kudziwa Mulungu.

  • 2 Petulo 1:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Nʼchifukwa chake sitikayikira ngakhale pangʼono kuti mawu aulosiwa adzakwaniritsidwa ndipo mukuchita bwino kuwaganizira mozama. Mawu amenewa aziwala mʼmitima yanu ngati nyale+ imene ikuwala mumdima. Pitirizani kuchita zimenezi mpaka mʼbandakucha, nthanda*+ itatuluka.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena