Yohane 8:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Yesu anawauza kuti: “Ndithudi ndikukuuzani, Abulahamu asanakhaleko, ine nʼkuti ndilipo kale.”+ Yohane 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiye tsopano Atate, ndiloleni kuti ndikhale pambali panu ndipo mundipatse ulemerero umene ndinali nawo pambali panu dziko lisanakhalepo.+
5 Ndiye tsopano Atate, ndiloleni kuti ndikhale pambali panu ndipo mundipatse ulemerero umene ndinali nawo pambali panu dziko lisanakhalepo.+