Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 3:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Mwana wanga, usakane malangizo* a Yehova+

      Ndipo usanyansidwe ndi kudzudzula kwake,+

  • Miyambo 4:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Gwira mwamphamvu malangizo ndipo usawasiye.+

      Uwasunge bwino chifukwa iwo ndi moyo wako.+

  • Aheberi 12:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Muyenera kupirira kuti muphunzitsidwe.* Mulungu akuchita nanu zinthu ngati ana ake.+ Ndi mwana wanji amene bambo ake samupatsa chilango?+

  • Aheberi 12:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Bambo athu otibereka ankatilanga ndipo tinkawalemekeza. Ndiye kuli bwanji Atate wa moyo wathu wauzimu? Kodi sitiyenera kuwagonjera koposa pamenepo kuti tikhale ndi moyo?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena