Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 7:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ine ndidzakhala bambo ake ndipo iye adzakhala mwana wanga.+ Akalakwitsa zinthu zina, ine ndidzamudzudzula ndi ndodo ya anthu ndi zikoti za ana a anthu.*+

  • Aheberi 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Zinthu zonse zinakhalapo kuti zipereke ulemerero kwa Mulungu komanso zinakhalapo kudzera mwa iye. Choncho kuti athandize ana ambiri kukhala ndi ulemerero,+ zinali zoyenera kuti achititse Mtumiki Wamkulu wachipulumutso chawo+ kukhala wangwiro kudzera mʼmavuto amene anakumana nawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena