Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 24:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Nzeru zimamanga nyumba ya* munthu,+

      Ndipo kuzindikira kumachititsa kuti ilimbe kwambiri.

  • Mateyu 7:24, 25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Choncho aliyense amene wamva mawu angawa nʼkuchita zimene wamvazo, adzafanana ndi munthu wanzeru, amene anamanga nyumba yake pathanthwe.+ 25 Ndiyeno kunagwa chimvula champhamvu ndipo madzi anasefukira. Kenako chimphepo chinawomba mwamphamvu, koma nyumbayo sinagwe chifukwa chakuti inakhazikika pathanthwepo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena