Miyambo 3:11, 12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwana wanga, usakane malangizo* a Yehova+Ndipo usanyansidwe ndi kudzudzula kwake,+12 Chifukwa Yehova amadzudzula munthu amene amamukonda,+Ngati mmene bambo amadzudzulira mwana amene amasangalala naye.+
11 Mwana wanga, usakane malangizo* a Yehova+Ndipo usanyansidwe ndi kudzudzula kwake,+12 Chifukwa Yehova amadzudzula munthu amene amamukonda,+Ngati mmene bambo amadzudzulira mwana amene amasangalala naye.+