Deuteronomo 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu mukudziwa bwino mumtima mwanu kuti Yehova Mulungu wanu ankakulangizani, ngati mmene bambo amalangizira mwana wake.+ Aheberi 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Muyenera kupirira kuti muphunzitsidwe.* Mulungu akuchita nanu zinthu ngati ana ake.+ Ndi mwana wanji amene bambo ake samupatsa chilango?+ Aheberi 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Bambo athu otibereka ankatilanga ndipo tinkawalemekeza. Ndiye kuli bwanji Atate wa moyo wathu wauzimu? Kodi sitiyenera kuwagonjera koposa pamenepo kuti tikhale ndi moyo?+
5 Inu mukudziwa bwino mumtima mwanu kuti Yehova Mulungu wanu ankakulangizani, ngati mmene bambo amalangizira mwana wake.+
7 Muyenera kupirira kuti muphunzitsidwe.* Mulungu akuchita nanu zinthu ngati ana ake.+ Ndi mwana wanji amene bambo ake samupatsa chilango?+
9 Bambo athu otibereka ankatilanga ndipo tinkawalemekeza. Ndiye kuli bwanji Atate wa moyo wathu wauzimu? Kodi sitiyenera kuwagonjera koposa pamenepo kuti tikhale ndi moyo?+