Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 13:8, 9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Choncho Abulamu anauza Loti+ kuti: “Chonde, pasakhale mkangano uliwonse pakati pa ine ndi iwe, komanso pakati pa abusa anga ndi abusa ako, pajatu ndife pachibale. 9 Tiye tisiyane. Ukhoza kusankha mbali iliyonse ya dzikoli. Iwe ukapita kumanzere, ine ndipita kumanja, koma ukapita kumanja, ine ndipita kumanzere.”

  • Miyambo 25:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Usamafulumire kupititsa mlandu kukhoti,

      Chifukwa udzachita chiyani mnzako akadzapereka umboni wosonyeza kuti iweyo ndi wolakwa?+

  • Mateyu 5:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Koma ine ndikukuuzani kuti: Musamalimbane ndi munthu woipa, koma wina akakumenyani mbama patsaya lakumanja, muzimupatsanso tsaya linalo.+

  • Aroma 12:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ngati nʼkotheka, yesetsani mmene mungathere kuti muzikhala mwamtendere ndi anthu onse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena