Salimo 18:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kwa munthu woyera, mumasonyeza kuti ndinu woyera,+Koma kwa munthu wopotoka maganizo mumasonyeza kuti ndinu wochenjera.+ Miyambo 6:14, 15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Popeza mtima wake ndi wachinyengo,Nthawi zonse amakonza ziwembu+ komanso amakhalira kuyambanitsa anthu.+ 15 Choncho tsoka lake lidzabwera mwadzidzidzi.Adzathyoledwa modzidzimutsa moti sadzachira.+
26 Kwa munthu woyera, mumasonyeza kuti ndinu woyera,+Koma kwa munthu wopotoka maganizo mumasonyeza kuti ndinu wochenjera.+
14 Popeza mtima wake ndi wachinyengo,Nthawi zonse amakonza ziwembu+ komanso amakhalira kuyambanitsa anthu.+ 15 Choncho tsoka lake lidzabwera mwadzidzidzi.Adzathyoledwa modzidzimutsa moti sadzachira.+