Miyambo 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndi bwino kudya mkate wouma pali mtendere,*+Kusiyana ndi kuchita maphwando ochuluka* mʼnyumba imene muli mikangano.+ Miyambo 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndi bwino kukhala mʼchipululuKusiyana ndi kukhala ndi mkazi wolongolola* komanso wosachedwa kukwiya.+ Miyambo 25:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndi bwino kukhala pakona ya denga la nyumbaKusiyana ndi kukhala mʼnyumba limodzi ndi mkazi wolongolola.*+ Miyambo 27:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mkazi wolongolola* ali ngati denga limene limadontha nthawi zonse pa tsiku la mvula.+
17 Ndi bwino kudya mkate wouma pali mtendere,*+Kusiyana ndi kuchita maphwando ochuluka* mʼnyumba imene muli mikangano.+
19 Ndi bwino kukhala mʼchipululuKusiyana ndi kukhala ndi mkazi wolongolola* komanso wosachedwa kukwiya.+
24 Ndi bwino kukhala pakona ya denga la nyumbaKusiyana ndi kukhala mʼnyumba limodzi ndi mkazi wolongolola.*+