Miyambo 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndi bwino kukhala pakona ya denga la nyumbaKusiyana ndi kukhala mʼnyumba limodzi ndi mkazi wolongolola.*+ Miyambo 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndi bwino kukhala mʼchipululuKusiyana ndi kukhala ndi mkazi wolongolola* komanso wosachedwa kukwiya.+
9 Ndi bwino kukhala pakona ya denga la nyumbaKusiyana ndi kukhala mʼnyumba limodzi ndi mkazi wolongolola.*+
19 Ndi bwino kukhala mʼchipululuKusiyana ndi kukhala ndi mkazi wolongolola* komanso wosachedwa kukwiya.+