Miyambo 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mʼnyumba ya munthu wolungama muli chuma chambiri,Koma zokolola za munthu woipa zimamubweretsera mavuto.+ Mlaliki 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Komanso Mulungu woona akapatsa munthu chuma ndiponso zinthu zambiri+ zimene angathe kusangalala nazo, ayenera kulandira mphoto yake* ndi kusangalala chifukwa cha ntchito imene waigwira mwakhama. Imeneyi ndi mphatso yochokera kwa Mulungu.+
6 Mʼnyumba ya munthu wolungama muli chuma chambiri,Koma zokolola za munthu woipa zimamubweretsera mavuto.+
19 Komanso Mulungu woona akapatsa munthu chuma ndiponso zinthu zambiri+ zimene angathe kusangalala nazo, ayenera kulandira mphoto yake* ndi kusangalala chifukwa cha ntchito imene waigwira mwakhama. Imeneyi ndi mphatso yochokera kwa Mulungu.+