Salimo 34:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Opani Yehova, inu oyera ake onse,Chifukwa onse amene amamuopa sasowa kanthu.+ Miyambo 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu asanagwe, mtima wake umadzikweza,+Ndipo akadzichepetsa amapeza ulemerero.+