Miyambo 27:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwana wanga, khala wanzeru ndipo usangalatse mtima wanga,+Kuti ndimuyankhe amene amanditonza.+ 3 Yohane 4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Palibe chimene chimandisangalatsa kwambiri* kuposa kumva kuti ana anga akuyendabe mʼchoonadi.+