Miyambo 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Miyambi ya Solomo.+ Mwana wanzeru amasangalatsa bambo ake,+Koma mwana wopusa amamvetsa chisoni mayi ake. Miyambo 23:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mwana wanga, mtima wako ukakhala wanzeru,Ndithu mtima wanga udzasangalala.+ 2 Yohane 4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndikusangalala kwambiri chifukwa ndapeza ena mwa ana anu akuyenda mʼchoonadi+ mogwirizana ndi lamulo limene tinalandira kwa Atate.
10 Miyambi ya Solomo.+ Mwana wanzeru amasangalatsa bambo ake,+Koma mwana wopusa amamvetsa chisoni mayi ake.
4 Ndikusangalala kwambiri chifukwa ndapeza ena mwa ana anu akuyenda mʼchoonadi+ mogwirizana ndi lamulo limene tinalandira kwa Atate.