Afilipi 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zinthu zimene munaphunzira, zimene munazivomereza, zimene munamva kwa ine komanso zimene munandiona ndikuchita, muzichita zimenezo+ ndipo Mulungu wamtendere adzakhala nanu.
9 Zinthu zimene munaphunzira, zimene munazivomereza, zimene munamva kwa ine komanso zimene munandiona ndikuchita, muzichita zimenezo+ ndipo Mulungu wamtendere adzakhala nanu.