Afilipi 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zinthu zimene munaphunzira, zimene munazivomereza, zimene munazimva, ndi zimene munaziona kwa ine, muzichita zimenezo,+ ndipo Mulungu wamtendere+ adzakhala nanu. Afilipi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:9 Nsanja ya Olonda,7/15/2005, ptsa. 24-259/1/1994, tsa. 1810/15/1989, tsa. 16
9 Zinthu zimene munaphunzira, zimene munazivomereza, zimene munazimva, ndi zimene munaziona kwa ine, muzichita zimenezo,+ ndipo Mulungu wamtendere+ adzakhala nanu.