Levitiko 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Usamadane ndi mʼbale wako mumtima mwako,+ koma uzimudzudzula+ kuti iwenso usakhale wochimwa ngati iyeyo. Mateyu 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Komanso ngati mʼbale wako wachimwa, upite kukamufotokozera zimene walakwitsazo* panokha, iwe ndi iyeyo.+ Ngati wakumvera, ndiye kuti wabweza mʼbale wakoyo.+
17 Usamadane ndi mʼbale wako mumtima mwako,+ koma uzimudzudzula+ kuti iwenso usakhale wochimwa ngati iyeyo.
15 Komanso ngati mʼbale wako wachimwa, upite kukamufotokozera zimene walakwitsazo* panokha, iwe ndi iyeyo.+ Ngati wakumvera, ndiye kuti wabweza mʼbale wakoyo.+