Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 18:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Dzina la Yehova ndi nsanja yolimba.+

      Wolungama amathawira mmenemo ndipo amatetezedwa.*+

  • Yesaya 26:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Inu anthu anga, pitani mukalowe mʼzipinda zanu zamkati,

      Ndipo mukatseke zitseko.+

      Mukabisale kwa kanthawi

      Mpaka mkwiyo utadutsa.*+

  • Aheberi 11:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Chifukwa cha chikhulupiriro, Nowa+ atachenjezedwa ndi Mulungu za zinthu zimene zinali zisanaoneke,+ anasonyeza kuopa Mulungu ndipo anamanga chingalawa+ kuti banja lake lipulumukiremo. Chifukwa cha chikhulupiriro, anatsutsa dziko+ ndipo anaonedwa kuti ndi wolungama chifukwa cha chikhulupirirocho.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena