Salimo 62:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komanso chikondi chokhulupirika ndi chanu, inu Yehova,+Chifukwa inu mumabwezera aliyense mogwirizana ndi zochita zake.+ Luka 18:6, 7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako Ambuye anati: “Mwamvatu zimene woweruzayo ananena ngakhale kuti anali wosalungama! 7 Ndiye kodi Mulungu sadzaonetsetsa kuti chilungamo chachitika kwa osankhidwa ake, amene amafuulira kwa iye masana ndi usiku,+ pamene akuwalezera mtima?+
12 Komanso chikondi chokhulupirika ndi chanu, inu Yehova,+Chifukwa inu mumabwezera aliyense mogwirizana ndi zochita zake.+
6 Kenako Ambuye anati: “Mwamvatu zimene woweruzayo ananena ngakhale kuti anali wosalungama! 7 Ndiye kodi Mulungu sadzaonetsetsa kuti chilungamo chachitika kwa osankhidwa ake, amene amafuulira kwa iye masana ndi usiku,+ pamene akuwalezera mtima?+