Yobu 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 nʼkunena kuti: “Ndinatuluka mʼmimba mwa mayi anga ndili wamaliseche,Ndipo ndidzabwerera ndilinso wamaliseche.+ Yehova wapereka,+ ndipo Yehova yemweyo watenga. Dzina la Yehova lipitirize kutamandidwa.”
21 nʼkunena kuti: “Ndinatuluka mʼmimba mwa mayi anga ndili wamaliseche,Ndipo ndidzabwerera ndilinso wamaliseche.+ Yehova wapereka,+ ndipo Yehova yemweyo watenga. Dzina la Yehova lipitirize kutamandidwa.”