Yobu 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye akalanda chinthu, ndani angalimbane naye? Ndani angamufunse kuti, ‘Mukuchita chiyani?’+ Yesaya 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wasankha zoti achite,Ndiye ndi ndani amene angazilepheretse?+ Dzanja lake latambasulidwa,Ndi ndani amene angalibweze?+
27 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wasankha zoti achite,Ndiye ndi ndani amene angazilepheretse?+ Dzanja lake latambasulidwa,Ndi ndani amene angalibweze?+