Salimo 33:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma zolinga za Yehova zidzakhalapo mpaka kalekale.+Maganizo amumtima mwake adzakhalapo ku mibadwomibadwo. Miyambo 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Munthu amakhala ndi mapulani ambiri mumtima mwake,Koma zolinga za Yehova nʼzimene zidzakwaniritsidwe.+ Miyambo 21:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Palibe nzeru kapena kuzindikira, kapena malangizo amene angalepheretse zimene Yehova amafuna.+ Yesaya 46:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndikuitana mbalame yodya nyama kuchokera kotulukira dzuwa,*+Ndikuitana munthu kuchokera kudziko lakutali kuti adzachite zolinga zanga.+ Ineyo ndalankhula ndipo ndidzazichita. Ndakonza kuti zimenezi zichitike komanso ndidzazichita.+
11 Koma zolinga za Yehova zidzakhalapo mpaka kalekale.+Maganizo amumtima mwake adzakhalapo ku mibadwomibadwo.
21 Munthu amakhala ndi mapulani ambiri mumtima mwake,Koma zolinga za Yehova nʼzimene zidzakwaniritsidwe.+
11 Ine ndikuitana mbalame yodya nyama kuchokera kotulukira dzuwa,*+Ndikuitana munthu kuchokera kudziko lakutali kuti adzachite zolinga zanga.+ Ineyo ndalankhula ndipo ndidzazichita. Ndakonza kuti zimenezi zichitike komanso ndidzazichita.+