Yobu 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Yobu anamuyankha kuti: “Ukulankhula ngati mmene amalankhulira akazi opusa. Kodi tizingolandira zabwino zokhazokha kuchokera kwa Mulungu woona osalandiranso zoipa?”+ Ngakhale kuti anakumana ndi zonsezi, Yobu sananene chilichonse cholakwika.*+ Yesaya 45:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndimapanga kuwala+ ndiponso ndimabweretsa mdima.+Ndimabweretsa mtendere+ komanso tsoka.+Ine Yehova ndimapanga zonsezi.
10 Koma Yobu anamuyankha kuti: “Ukulankhula ngati mmene amalankhulira akazi opusa. Kodi tizingolandira zabwino zokhazokha kuchokera kwa Mulungu woona osalandiranso zoipa?”+ Ngakhale kuti anakumana ndi zonsezi, Yobu sananene chilichonse cholakwika.*+
7 Ndimapanga kuwala+ ndiponso ndimabweretsa mdima.+Ndimabweretsa mtendere+ komanso tsoka.+Ine Yehova ndimapanga zonsezi.