-
Ekisodo 1:13, 14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Choncho Aiguputo anakakamiza Aisiraeli kuti azigwira ntchito yaukapolo mwankhanza.+ 14 Iwo anasautsa moyo wa Aisiraeliwo powagwiritsa ntchito yowawa, yomwe inali yoponda matope ndi kuumba njerwa. Anawagwiritsa ntchito yaukapolo wa mtundu uliwonse mʼmunda. Ankawazunza komanso kuwagwiritsa ntchito ya mtundu uliwonse wa ukapolo.+
-