Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mlaliki 2:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Palibe chabwino kwa munthu kuposa kuti adye, amwe ndi kusangalala chifukwa choti wagwira ntchito mwakhama.+ Ndinazindikira kuti zimenezinso nʼzochokera mʼdzanja la Mulungu woona,+

  • Mlaliki 3:12, 13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndazindikira kuti palibe chabwino kuposa kuti iwo asangalale ndiponso kuti azichita zabwino pamene ali ndi moyo,+ 13 komanso kuti munthu aliyense adye ndi kumwa nʼkumasangalala ndi zinthu zabwino, chifukwa cha ntchito yake yonse imene waigwira mwakhama. Imeneyi ndi mphatso yochokera kwa Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena