Yobu 28:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma kodi nzeru zingapezeke kuti?+Ndipo kumvetsa zinthu kumachokera kuti?+ Mlaliki 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Zimene zinachitika kale sitingathe kuzimvetsa ndipo nʼzozama kwambiri. Ndi ndani angazimvetse?+ Mlaliki 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwe sudziwa mmene mzimu umachititsira kuti mafupa a mwana amene ali mʼmimba mwa mayi ake akule.+ Mofanana ndi zimenezi sudziwanso ntchito ya Mulungu woona, amene amachita zinthu zonse.+
5 Iwe sudziwa mmene mzimu umachititsira kuti mafupa a mwana amene ali mʼmimba mwa mayi ake akule.+ Mofanana ndi zimenezi sudziwanso ntchito ya Mulungu woona, amene amachita zinthu zonse.+