Deuteronomo 33:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye ankakonda anthu ake,+Anthu oyera onsewa ali mʼmanja mwanu.+ Iwowa anakhala pamapazi anu.+Anayamba kumvetsera mawu anu.+ 1 Samueli 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amateteza mapazi a okhulupirika ake,+Koma anthu oipa adzawakhalitsa chete mumdima,+Popeza munthu sapambana chifukwa cha mphamvu zake.+ Salimo 37:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Lola kuti Yehova akutsogolere panjira yako,*+Uzimudalira ndipo iye adzakuthandiza.+
3 Iye ankakonda anthu ake,+Anthu oyera onsewa ali mʼmanja mwanu.+ Iwowa anakhala pamapazi anu.+Anayamba kumvetsera mawu anu.+
9 Amateteza mapazi a okhulupirika ake,+Koma anthu oipa adzawakhalitsa chete mumdima,+Popeza munthu sapambana chifukwa cha mphamvu zake.+