Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 12:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Inuyo ndi mabanja anu muzidzadya zimenezi kumalo amenewo pamaso pa Yehova Mulungu wanu,+ ndipo muzidzasangalala ndi zochita zanu zonse+ chifukwa Yehova Mulungu wanu wakudalitsani.

  • Salimo 104:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Komanso kuti mutuluke vinyo amene amasangalatsa mtima wa munthu,+

      Mafuta amene amachititsa kuti nkhope ya munthu isalale,

      Ndiponso chakudya chimene chimapereka mphamvu kwa munthu.*+

  • Mlaliki 2:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Palibe chabwino kwa munthu kuposa kuti adye, amwe ndi kusangalala chifukwa choti wagwira ntchito mwakhama.+ Ndinazindikira kuti zimenezinso nʼzochokera mʼdzanja la Mulungu woona,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena