Genesis 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Udzadya chakudya kuchokera mʼthukuta la nkhope yako mpaka utabwerera kunthaka, chifukwa nʼkumene unatengedwa.+ Popeza ndiwe fumbi, kufumbiko udzabwerera.”+ Salimo 146:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mpweya* wake umachoka, ndipo iye amabwerera kunthaka.+Pa tsiku limenelo zonse zimene amaganiza zimatheratu.+
19 Udzadya chakudya kuchokera mʼthukuta la nkhope yako mpaka utabwerera kunthaka, chifukwa nʼkumene unatengedwa.+ Popeza ndiwe fumbi, kufumbiko udzabwerera.”+
4 Mpweya* wake umachoka, ndipo iye amabwerera kunthaka.+Pa tsiku limenelo zonse zimene amaganiza zimatheratu.+