1 Yohane 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kukonda Mulungu kumatanthauza kutsatira malamulo ake,+ ndipo malamulo akewo si ovuta kuwatsatira.+