Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 14:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Nzeru zimathandiza munthu wochenjera kuzindikira njira imene akuyenda,

      Koma anthu opusa amapusitsika* ndi kupusa kwawo komwe.+

  • Miyambo 17:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Munthu wozindikira amakhala ndi cholinga choti apeze nzeru,

      Koma maso a munthu wopusa amangoyendayenda mpaka kumalekezero a dziko lapansi.+

  • Yohane 3:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Kuwala kwafika mʼdziko+ koma mʼmalo mokonda kuwala anthu akukonda mdima popeza ntchito zawo nʼzoipa, nʼchifukwa chake adzaweruzidwe.

  • 1 Yohane 2:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma amene amadana ndi mʼbale wake ali mumdima ndipo akuyenda mumdimawo+ komanso sakudziwa kumene akupita+ popeza maso ake sakuona chifukwa cha mdimawo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena