1 Yohane 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ngati wina amanena kuti, “Ndimakonda Mulungu,” koma nʼkumadana ndi mʼbale wake,+ ndiye kuti ndi wabodza. Chifukwa amene sakonda mʼbale wake+ amene amamuona, sangakonde Mulungu amene sanamuonepo.+
20 Ngati wina amanena kuti, “Ndimakonda Mulungu,” koma nʼkumadana ndi mʼbale wake,+ ndiye kuti ndi wabodza. Chifukwa amene sakonda mʼbale wake+ amene amamuona, sangakonde Mulungu amene sanamuonepo.+