Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 30:23, 24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 “Kenako utenge mafuta onunkhira, abwino kwambiri awa: mule* woundana wokwana masekeli 500, sinamoni wonunkhira bwino hafu ya muyezo wa mule, kapena kuti masekeli 250, ndi kalamasi wonunkhira wokwana masekeli 250. 24 Utengenso kasiya* masekeli 500 ofanana ndi masekeli akumalo oyera*+ komanso hini* imodzi ya mafuta a maolivi.

  • Ekisodo 30:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Utenge muyezo wofanana wa zinthu zonunkhira izi:+ madontho a sitakate,* onika, mafuta onunkhira a galibanamu ndi lubani* weniweni.

  • Ezekieli 27:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Iwe mwana wa munthu, imba nyimbo yoimba polira yokhudza Turo.+

  • Ezekieli 27:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Unkachita malonda ndi amalonda a ku Sheba ndi ku Raama.+ Iwo anakupatsa mafuta onunkhira abwino kwambiri amitundu yosiyanasiyana, miyala yamtengo wapatali komanso golide posinthanitsa ndi katundu wako.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena