Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 10:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Mahatchi a Solomo ankawagula kuchokera ku Iguputo ndipo gulu la amalonda a mfumu linkagula mahatchiwo mʼmagulumagulu.*+

  • 2 Mbiri 1:16, 17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Mahatchi a Solomo ankawagula kuchokera ku Iguputo+ ndipo gulu la amalonda a mfumu linkagula mahatchiwo mʼmagulumagulu.*+ 17 Galeta lililonse lochokera ku Iguputo mtengo wake unali ndalama zasiliva 600 pomwe mtengo wa hatchi unali ndalama zasiliva 150. Ndipo iwo ankagulitsa zinthuzi kwa mafumu onse a Ahiti ndi mafumu a ku Siriya.

  • Nyimbo ya Solomo 6:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 “Wokondedwa wangawe,+ ndiwe wokongola ngati Tiriza,*+

      Ndiwe wooneka bwino ngati Yerusalemu,+

      Ndipo ndiwe wogometsa ngati magulu a asilikali amene azungulira mbendera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena