Numeri 21:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho Aisiraeli analanda mizinda yonseyi nʼkuyamba kukhala mʼmizinda yonse ya Aamori+ ku Hesiboni ndi mʼmidzi yake yonse yozungulira. Yoswa 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho Aisiraeli anachita maere nʼkupatsa Alevi mizinda imeneyi ndi malo ake odyetserako ziweto, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula kudzera mwa Mose.+ Yoswa 21:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Hesiboni+ ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso Yazeri+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse inalipo mizinda 4.
25 Choncho Aisiraeli analanda mizinda yonseyi nʼkuyamba kukhala mʼmizinda yonse ya Aamori+ ku Hesiboni ndi mʼmidzi yake yonse yozungulira.
8 Choncho Aisiraeli anachita maere nʼkupatsa Alevi mizinda imeneyi ndi malo ake odyetserako ziweto, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula kudzera mwa Mose.+
39 Hesiboni+ ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso Yazeri+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse inalipo mizinda 4.