Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 10:15, 16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kanani anabereka Sidoni,+ mwana wake woyamba, kenako anabereka Heti.+ 16 Analinso kholo la Ayebusi,+ Aamori,+ Agirigasi,

  • Genesis 15:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Koma mʼbadwo wa 4 wa mbadwa zako ndi umene udzabwerere kuno,+ chifukwa nthawi yoti Aamori alangidwe sinakwane.”*+

  • Ekisodo 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Choncho ndipita kuti ndikawapulumutse mʼmanja mwa Aiguputo+ ndi kuwatulutsa mʼdzikolo nʼkuwalowetsa mʼdziko labwino komanso lalikulu, dziko loyenda mkaka ndi uchi.+ Ndiwalowetsa mʼdziko la Akanani, Ahiti, Aamori, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi.+

  • Deuteronomo 7:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Yehova Mulungu wanu akadzakulowetsani mʼdziko limene mwatsala pangʼono kulitenga kuti likhale lanu,+ adzakuchotseraninso mitundu ikuluikulu.+ Adzakuchotserani Ahiti, Agirigasi, Aamori,+ Akanani, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi,+ mitundu 7 ikuluikulu komanso yamphamvu kuposa inu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena