Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 21:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Zitatero, Abulahamu anadzala mtengo wa bwemba pa Beere-seba, ndipo kumeneko anaitanira pa dzina la Yehova,+ Mulungu yemwe adzakhalepo mpaka kalekale.+

  • Salimo 90:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Mapiri asanabadwe,

      Kapena musanakhazikitse dziko lapansi komanso nthaka,+

      Inu ndinu Mulungu kuyambira kalekale mpaka kalekale.+

  • Yeremiya 10:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma Yehova ndi Mulungu woonadi.

      Iye ndi Mulungu wamoyo+ ndipo ndi Mfumu yamuyaya.+

      Dziko lapansi lidzagwedezeka chifukwa cha mkwiyo wake,+

      Ndipo palibe mitundu ya anthu imene idzapilire mkwiyo wake.

  • 1 Timoteyo 1:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Kwa Mulungu yekhayo+ yemwe ndi Mfumu yamuyaya,+ amene saafa+ komanso wosaoneka,+ kukhale ulemu ndi ulemerero mpaka kalekale. Ame.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena