Genesis 30:22, 23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Potsirizira pake, Mulungu anakumbukira Rakele ndipo anamva pemphero lake nʼkumuthandiza kuti ayambe kubereka.*+ 23 Rakele anakhala woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna. Ndiyeno iye anati: “Mulungu wachotsa kunyozeka kwanga.”+ Luka 1:24, 25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Patapita masiku angapo, mkazi wake Elizabeti anakhala woyembekezera ndipo anakhala kwayekha miyezi 5. Iye ananena kuti: 25 “Izitu nʼzimene Yehova* wandichitira masiku ano. Iye wandikumbukira kuti achotse kunyozeka kwanga pamaso pa anthu.”+
22 Potsirizira pake, Mulungu anakumbukira Rakele ndipo anamva pemphero lake nʼkumuthandiza kuti ayambe kubereka.*+ 23 Rakele anakhala woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna. Ndiyeno iye anati: “Mulungu wachotsa kunyozeka kwanga.”+
24 Patapita masiku angapo, mkazi wake Elizabeti anakhala woyembekezera ndipo anakhala kwayekha miyezi 5. Iye ananena kuti: 25 “Izitu nʼzimene Yehova* wandichitira masiku ano. Iye wandikumbukira kuti achotse kunyozeka kwanga pamaso pa anthu.”+