Deuteronomo 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Yehova anakutulutsani ndi dzanja lamphamvu kuti akulanditseni mʼnyumba yaukapolo,+ mʼmanja mwa Farao* mfumu ya Iguputo, chifukwa chakuti Yehova anakukondani, komanso chifukwa chosunga lumbiro lake limene analumbirira makolo anu.+ Yeremiya 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova anaonekera kwa ine ali kutali ndipo anati: “Ine ndakukonda ndipo ndidzakukonda mpaka kalekale. Nʼchifukwa chake ndakukokera kwa ine ndi chikondi chokhulupirika.*+
8 Koma Yehova anakutulutsani ndi dzanja lamphamvu kuti akulanditseni mʼnyumba yaukapolo,+ mʼmanja mwa Farao* mfumu ya Iguputo, chifukwa chakuti Yehova anakukondani, komanso chifukwa chosunga lumbiro lake limene analumbirira makolo anu.+
3 Yehova anaonekera kwa ine ali kutali ndipo anati: “Ine ndakukonda ndipo ndidzakukonda mpaka kalekale. Nʼchifukwa chake ndakukokera kwa ine ndi chikondi chokhulupirika.*+