Yesaya 44:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova, Mfumu ya Isiraeli,+ amene anawawombola,+Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, wanena kuti: ‘Ine ndine woyamba ndi womaliza.+ Ndipo palibenso Mulungu wina kupatulapo ine.+ Yesaya 63:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Inutu ndinu Atate wathu.+Ngakhale kuti Abulahamu sankatidziwaNdipo Isiraeli sangatizindikire,Inu Yehova ndinu Atate wathu. Dzina lanu ndinu Wotiwombola wakalekale.+
6 Yehova, Mfumu ya Isiraeli,+ amene anawawombola,+Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, wanena kuti: ‘Ine ndine woyamba ndi womaliza.+ Ndipo palibenso Mulungu wina kupatulapo ine.+
16 Inutu ndinu Atate wathu.+Ngakhale kuti Abulahamu sankatidziwaNdipo Isiraeli sangatizindikire,Inu Yehova ndinu Atate wathu. Dzina lanu ndinu Wotiwombola wakalekale.+